Mawu Amunsi
a Abale na alongo athu ena cimawavuta kukhulupilila kuti Yehova amawakonda. M’nkhani ino, tikambilane cifukwa cake tingakhale otsimikiza kuti Yehova amakonda aliyense wa ife payekha. Tikambilanenso mmene tingagonjetsele zikayiko zilizonse zimene tingakhale nazo zokhudza cikondi cake pa ife.