Mawu Amunsi
c MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Paulo asanakhale Mkhristu, anaponya Akhristu ambili m’ndende. Koma atayamikila zimene Yesu anam’citila, anasintha na kulimbikitsa abale ake auzimu, amene n’kutheka kuti ena anali acibale kwa anthu amene iye anawazunza.