Mawu Amunsi
c MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: (kucoka pamwamba kupita pansi): Mwamuna na mkazi wake akulalikila m’dela limene n’zovuta kupeza anthu panyumba. Mwininyumba woyamba ali ku nchito, waciŵili ali ku cipatala, ndipo wacitatu akugula zinthu m’sitolo. Ofalitsawo afikila mwininyumba woyamba pa nthawi ina pa tsikulo. Akambilana na mwininyumba waciŵili pamene akucita ulaliki wapoyela pafupi na cipatala. Iwo akambilana na mwininyumba wacitatu mwa kum’tumila foni.