Mawu Amunsi
a Tikukhala m’nthawi zovuta, koma Yehova amatipatsa thandizo lofunikila kuti tipilile. M’nkhani ino, tidzaona mmene Yehova anathandizila mtumwi Paulo na Timoteyo kupitiliza kum’tumikila ngakhale kuti anali kukumana na mavuto. Tidzakambilana zinthu zinayi zimene Yehova watipatsa pofuna kutithandiza kupilila masiku ano.