Mawu Amunsi
a Nkhani ino ifotokoze mmene Yesu anathandizila anthu kukhala ophunzila ake, na zimene tingacite kuti titengele citsanzo cake. Tikambilanenso mbali zina za buku latsopano lakuti Kondwelani na Moyo kwamuyaya! Bukuli linakonzedwa na colinga cothandiza maphunzilo athu a Baibo kupita patsogolo mpaka kukabatizika.