Mawu Amunsi
b Mungapezenso zocitika zeni-zeni (1) mu Buku lofufuzila nkhani la Mboni za Yehova pansi pa mutu wakuti “Baibo,” pa kamutu kakuti “Ubwino wake,” ndiyeno pa kamutu kakuti “‘Baibulo Limasintha Anthu’ (Nkhani za mu Msanja ya Mlonda)” kapena (2) pa JW Laibulali® pa media pa mbali yakuti “Zocitika na Kufunsa Mafunso.”