Mawu Amunsi
a Kodi nthawi zina mumasungulumwa? Ngati n’conco, khalani wotsimikiza kuti Yehova amadziŵa mmene mumamvelela, ndipo amafuna kukuthandizani. M’nkhani ino, tikambilane zimene mungacite polimbana na vuto la kusungulumwa. Tiphunzilenso zimene tingacite polimbikitsa alambili anzathu amene amasungulumwa.