Mawu Amunsi
a Satana ali monga wosaka nyama waluso. Amafuna kutikola m’misampha yake kaya tatumikila Yehova kwa nthawi yaitali motani. M’nkhani ino, tiphunzile mmene Satana amaseŵenzetsela kunyada ndiponso dyela kuwononga ubale wathu na Mulungu. Tionenso zimene tingaphunzile ku zitsanzo za ena amene anagwidwapo mu msampha wa kunyada komanso dyela. Ndiponso tione mmene tingapewele misampha imeneyo.