Mawu Amunsi
b KUFOTOKOZELA MAWU ENA: Nkhani ino idzafotokoza kwambili za kunyada. Munthu akakhala na khalidwe limeneli amadziona kuti ni wofunika kwambili kuposa ena. Idzafotokozanso kwambili za dyela, kutanthauza cikhumbo cosalamulilika cofuna kukhala na ndalama zambili, mphamvu zoculuka, cilako-lako cosalamulilika ca kugonana, kapena zina zotelo.