Mawu Amunsi
d MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Mngelo wa Mulungu komanso Mfumu Uziya anakhala onyada. Dyela ndilo linapangitsa Hava kudya cipatso ca mu mtengo woletsedwa, linapangitsanso Davide kucita cigololo na Batiseba, komanso Yudasi kuba ndalama.