Mawu Amunsi
a Yehova watipatsa nchito yolalikila anthu, komanso kuwaphunzitsa kusunga zinthu zonse zimene Yesu anatilamula. Kodi n’ciani cimatilimbikitsa kuphunzitsa ena? Timakumana na zopinga zotani pa nchito yolalikila na kupanga ophunzila? Nanga tingazigonjetse bwanji zopinga zimenezo? Nkhani ino, iyankha mafunso amenewa.