Mawu Amunsi
a Okalamba okhulupilika ali ngati cuma camtengo wapatali. Nkhani ino, itithandiza kukulitsa ciyamikilo cathu pa okalamba. Cina, tikambilane mmene tingapindulile na nzelu zawo, komanso zimene akwanitsa kucita potumikila Mulungu. Idzalimbikitsanso okalamba kuona kuti ni ofunika m’gulu la Mulungu.