Mawu Amunsi
a M’mipingo yathu, tili na anyamata na atsikana ambili amene amayesetsa kucilikiza gulu la Yehova. Okalamba mu mpingo, mosasamala kanthu za cikhalidwe cawo, angathandize acinyamata kuseŵenzetsa mphamvu zawo mokwanila potumikila Yehova.