Mawu Amunsi
a Nkhani ino, ifotokoza kamvedwe katsopano ka lemba la Hagai 2:7. M’nkhani ino, tiphunzile mmene tingatengeleko mbali m’nchito yofunika kwambili imene ikugwedeza mitundu yonse. Tidzaonanso kuti nchito yogwedeza imeneyi imapangitsa anthu ena kumvetsela uthenga wathu, pamene ena amaukana.