Mawu Amunsi
c Kumeneku ni kusintha kwa kamvedwe kathu. Kale tinali kukhulupilila kuti kugwedeza mitundu yonse, si ndiko kupangitsa anthu oona mtima kuyamba kutumikila Yehova. Onani nkhani yakuti “Mafunso Ocokela kwa Oŵelenga,” mu Nsanja ya Olonda ya May 15, 2006.