Mawu Amunsi
a Cimaŵaŵa kwambili wa m’banja lathu akasiya Yehova. M’nkhani ino, tiona mmene Mulungu wathu amamvelela izi zakacitika. Tikambilane zimene acibale okhulupilika m’banjalo angacite kuti apilile cisoni, na kukhalabe olimba mwauzimu. Tikambilanenso zimene onse mu mpingo angacite kuti atonthoze na kuthandiza banja lokhudzidwalo.