Mawu Amunsi
a M’nkhani ino, tikambilane dongosolo la kulambila koona limene Yesu anakhazikitsa, komanso mmene Akhristu oyambilila anatsatilila dongosolo limenelo. Tionenso mmene Mboni za Yehova nazonso zimatsatilila kulambila koona kumeneko masiku ano.