Mawu Amunsi
a Timayembekezela mwacidwi mapeto a dongosolo lino la zinthu. Koma nthawi zina, tingakayikile ngati cikhulupililo cathu cidzakhala colimba, kuti tikakwanitse kupilila pa nthawi yovutayo. M’nkhani ino, tikambilane zitsanzo za ena, komanso zimene tiphunzilapo zotithandiza kutilimbitsa cikhulupililo cathu.