Mawu Amunsi
a Kodi cikondi cosasintha n’ciani? Kodi Yehova amaonetsa ndani cikondi cosasintha cimeneci? Nanga awo amene amaonetsedwa cikondi cotelo amapindula motani? Tidzakambilana mayankho pa mafunso amenewa, m’nkhani ziŵili zoyambilila zimene zifotokoza khalidwe lofunika kwambili limeneli.