Mawu Amunsi
c MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Yehova amaonetsa cikondi anthu onse, kuphatikizapo atumiki ake. Tumapikica tuli pa cithunzici tuonetsa njila zimene Yehova waonetsela cikondi kwa anthu onse. Njila yaikulu imene watiolnetsela cikondi, ni dipo imene anapeleka kuti tipindule.