Mawu Amunsi
d MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Anthu amene amakhala atumiki a Yehova na kuika cikhulupililo cawo mu dipo, iye amawasamalila mwapadela. Mulungu amaonetsa cikondi kwa anthu onse, koma atumiki ake amawaonetsanso cikondi cake cosasintha. Zitsanzo zake zikuonekela pa cithunzi.