Mawu Amunsi
a Akhristu sali pansi pa Cilamulo ca Mose. Komabe, cilamuloco cimachula zinthu zambili zimene tiyenela kucita komanso kupewa. Kudziŵa zinthuzo kudzatithandiza kukonda anthu, na kukondweletsa Mulungu. Nkhani ino, ifotokoza mmene tingapindulile na maphunzilo amene titengamo m’buku la Levitiko caputala 19.