Mawu Amunsi
a Yesu anatilimbikitsa kuloŵa pa cipata copapatiza cotsogolela ku njila yopita ku moyo. Iye anatilamulanso kukhazikitsa mtendele na Akhristu anzathu. Kodi tingakumane na zovuta ziti poseŵenzetsa malangizo amenewa? Nanga tingazigonjetse bwanji?