Mawu Amunsi
a Yakobo anakulila m’banja limodzi na Yesu. Iye anam’dziŵa bwino Mwana wa Mulungu wangwilo kuposa anthu ambili panthawiyo. M’nkhani ino, tiona zimene tingaphunzile pa umoyo wa Yakobo mng’ono wa Yesu, na zimene anaphunzitsa. Iye anadzakhala mzati mu mpingo wacikhristu m’nthawi ya atumwi.