Mawu Amunsi
a Anthu a Yehova amadziŵa kuti kumvela uphungu wozikika m’Baibo n’kopindulitsa. Koma panthawi imodzimodzi, si copepuka kulandila uphungu na kuugwilitsila nchito. N’cifukwa ciani zili conco? Nanga n’ciani cingatithandize kupindula na uphungu umene tapatsidwa?