Mawu Amunsi
a Nthawi zonse, Yesu anali kuika zabwino za ena patsogolo pa zofuna zake. M’nkhani ino, tikambilane mmene tingatengele citsanzo cake. Tikambilanenso mapindu amene tidzapeza tikatengela mzimu wodzimana wa Yesu.