Mawu Amunsi
b MAWU OFOTOKOZELA CITHUNZI: Dan m’bale wacinyamata, akuyang’ana pamene akulu aŵili abwela kudzaona atate ake ku cipatala. Citsanzo ca akulu amenewa cikumulimbikitsa kuti nayenso afunefune mipata yothandizila ena mu mpingo. M’bale wina wacinyamata Ben, akuona zimene Dan akucita. Citsanzo ca Dan cikulimbikitsa Ben kuthandiza kuyeletsa nawo Nyumba ya Ufumu.