Mawu Amunsi
a Kaya cikhalidwe cathu cotani, n’zotheka kuvala “umunthu watsopano.” Kuti ticite zimenezi, tiyenela kupitiliza kusintha kaganizidwe kathu na kuyesetsa kukhala monga Yesu. M’nkhani ino, tikambilane maganizo a Yesu komanso zocita zake. Tikambilanenso mmene tingapitilizile kutengela citsanzo cake pambuyo pa ubatizo.