Mawu Amunsi
a Pokhala Mlengi wa zinthu zonse, Yehova ni woyenela kum’lambila. Iye amavomeleza kulambila kwathu tikamamvela malamulo ake, na kutsatila mfundo zake. M’nkhani ino, tikambilane mbali 8 zokhudza kulambila. Pamene tikambilana, onani mmene tingawongolele pa mbalizo, komanso mmene zidzawonjezela cimwemwe cathu.