Mawu Amunsi
a Timapindula kwambili na nchito zimene akulu acikondi amagwila mwakhama kuti atithandize. M’nkhani ino, tikambilane zovuta zinayi zimene iwo amakumana nazo. Tikambilanenso mmene citsanzo ca mtumwi Paulo, cingawathandizile kugonjetsa zovuta zimenezo. Cina, idzalimbikitsa tonsefe kuonetsa akulu cifundo na cikondi, komanso kuwacilikiza pa utumiki wawo.