Mawu Amunsi
c Mosiyana na cilombo coyamba, cifanizilo cimeneci cilibe zisoti zacifumu ku nyanga zake. (Chiv. 13:1) Izi zili conco cifukwa ‘cikutuluka mwa mafumu 7 aja,’ ndipo cimapatsidwa mphamvu kucokela kwa mafumuwo.—Onani nkhani yakuti, “Kodi Cilombo Cofiila Kwambili Comwe Cimachulidwa M’caputala 17 ca Chivumbulutso Cimaimila Ciyani?” Nkhaniyi mungaipeze pa webusaiti ya jw.org ku Chichewa.