Mawu Amunsi
a Ino ni nkhani yothela pa nkhani zogwilizana zokhudza buku la Chivumbulutso. Monga tionele m’nkhani ino, amene adzakhalabe okhulupilika kwa Yehova adzakhala na tsogolo labwino. Koma amene amatsutsa ulamulilo wa Mulungu mapeto awo adzakhala ocititsa manyazi.