Mawu Amunsi
d MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: John na Tom ni abale acinyamata amene ali mu mpingo umodzi. John amathela nthawi yoculuka kusamalila motoka yake. Koma Tom amaseŵenzetsa motoka yake pothandiza ena kuyenda mu ulaliki na kupita ku misonkhano yampingo.