Mawu Amunsi
e MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: John amaseŵenza ovataimu. Iye safuna kukhumudwitsa abwana ake. Conco, nthawi iliyonse abwana ake akamuuza kuti agwile ovataimu John amavomela. Koma madzulo amodzi-modziwo, Tom, amene ni mtumiki wothandiza, wapita ku ulendo waubusa na mkulu wina. Kumbuyoku, Tom anauza abwana ake kuti madzulo alionse amapatula nthawi yocita zinthu zokhudza kulambila Yehova.