Mawu Amunsi
a M’mawu ake, Yehova amatitsimikizila kuti iye ni wokonzeka kukhululukila anthu ocimwa amene alapa. Koma nthawi zina, tingaone kuti sindife oyenela cikhululuko cake. M’nkhani ino, tikambilane cifukwa cake tingakhale otsimikiza kuti Mulungu wathu, nthawi zonse amakhala wokonzeka kutikhululukila tikalapadi macimo athu mocokela pansi pamtima.