Mawu Amunsi
c KUFOTOKOZELA MAWU ENA: “Kulapa” kumatanthauza kusintha kaganizidwe, kophatikizapo kudzimvela cisoni pa zoipa zimene munthu anacita, kapena zimene analephela kucita. Kulapa kwenikweni kumabala zipatso zabwino mwa munthuyo, zimene ni kusintha umoyo wake.