Mawu Amunsi
a Yehova ni wofunitsitsa kukhululukila ocimwa olapa. Pokhala Akhristu, timafuna kutengela citsanzo cake wina akatikhumudwitsa. M’nkhani ino, tikambilane macimo a anthu ŵena amene ife tingakhululuke, komanso macimo amene tiyenela kuuza akulu. Tikambilanenso cifukwa cake Yehova amafuna kuti tizikhululukilana, ndiponso madalitso amene tidzapeza tikacita zimenezo.