Mawu Amunsi
a Kuti tiumvetsetse bwino uthenga wa m’Baibo, tiyenela kumvetsa ulosi wa pa Genesis 3:15. Kuphunzila ulosi umenewu kungalimbitse cikhulupililo cathu mwa Yehova, na kutithandiza kukhala otsimikiza kuti iye adzakwanilitsa malonjezo ake onse.