Mawu Amunsi a Nthawi zina, M’bale Rutherford analil kucedwa “Woweluza” cifukwa anagwilapo nchito yoweluza ku Missouri, America.