Mawu Amunsi
a Baibo imalangiza Akhristu kuti azimvela olamulila akulu-akulu, kutanthauza maboma a m’dzikoli. Koma maboma ena amatsutsa Yehova poyela na atumiki ake. Kodi tingatani kuti tizimvela olamulila amenewo, koma panthawi imodzimodzi n’kukhalabe okhulupilika kwa Yehova?