Mawu Amunsi b Pa nthawi imene Yesu anabatizika na kudzozedwa na mzimu woyela, iye anayamba kukumbukila zinthu zonse zokhudza nthawi imene anali kumwamba asanabwele padziko lapansi.—Mat. 3:16.