Mawu Amunsi
d Mungapeze malingalilo ena okuthandizani kudziŵa zimene mungakambe kapena kucita kuti mutonthoze acisoni kaamba ka imfa, mu Nsanja ya Olonda ya Chichewa ya November 1, 2010. Nkhani yake ni yakuti “Muzitonthoza Anthu Amene Aferedwa, Ngati Mmene Yesu Anachitira.”