Mawu Amunsi
d Onani nyimbo zotsatilazi m’buku lakuti ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova: “Yelekeza Uli M’dziko Latsopano” (Nyimbo 139), “Yang’ana pa Mphoto” (Nyimbo 144), “Adzaitana” (Nyimbo 151). Onaninso pa jw.org nyimbo zopekedwa koyamba zakuti “Dziko Latsopano Ili Pafupi Kwambili,” “Dziko Latsopano Likubwelalo,” komanso yakuti “Bwelani M’dzaone.”