Mawu Amunsi
b Baibo imachula nthawi ziŵili pomwe Aisiraeli anapeleka nsembe kwa Yehova m’cipululu. Nthawi yoyamba inali pamene anali kudzoza ansembe ndiponso pomwe anali kucita Pasika. Zocitika zonsezi zinacitika m’caka ca 1512 B.C.E., comwe cinali caka caciŵili kucokela pomwe Aisiraeli anatuluka mu Iguputo—Lev. 8:14–9:24; Num. 9:1-5.