Mawu Amunsi
c Cakumapeto kwa ulendo wawo wa zaka 40 wa m’cipululu, Aisiraeli anafunkha nyama masauzande ambili kunkhondo. (Num 31:32-34) Ngakhale n’telo, iwo anapitiliza kudya mana mpaka ataloŵa m’Dziko Lolonjezedwa.—Yos 5:10-12.