Mawu Amunsi
d Palibe ciliconse coonetsa kuti nyama nazonso zinali kudya mana. Yehova anawauza kuti aliyense azitolela mana mogwilizana na muyeso umene angadye ndipo sanachulepo za nyama.—Eks 16:15, 16.