Mawu Amunsi
a M’Malemba a Ciheberi mulibe mawu akuti “wokhwima” komanso “wosakhwima,” koma muli mawu amene amapeleka lingalilo lofanana na mawu amenewa. Mwa citsanzo, buku la Miyambo limasiyanitsa mnyamata wosadziŵa zinthu na mnyamata wanzelu komanso wodziŵa zinthu.—Miy. 1:4, 5.