Mawu Amunsi
a Lamulo la Mulungu lopezeka pa Deuteronomy 23:3-6 inaletsa a Amoni komanso Amowabu kuloŵa mu mpingo wa Aisiraeli. Zioneka kuti lamulo limeneli linali kuwaletsa kukhala nzika za Isiraeli mwalamulo. Komabe, silinawaletse kugwilizana na anthu a Mulungu kapena kupezeka pakati pawo. Onani buku lakuti Insight on the Scriptures, Volume 1, tsamba 95.