Mawu Amunsi
d M’zikhalidwe zina, kambili m’bale ndiye amafunsila mlongo. Komabe, sikulakwa mlongo kufikila m’bale. (Rute 3:1-13) Kuti mudziŵe zambili pa nkhaniyi, onani nkhani yakuti, “Acinyamata Akufunsa Kuti . . . Kodi Mnyamata Ndingamuuze Bwanji Kuti Ndikumufuna?” mu Galamukani! ya November 8, 2004.