Mawu Amunsi
c MAWU OFOTOKOZELA CITHUNZI: Zifukwa zitatu zoonetsa kuti n’zosatheka kufikila munthu aliyense pa nchito yathu yolalikila: (1) Mzimayi akukhala ku dziko kumene kulalikila n’koopsa cifukwa ca cipembedzo ca kumeneko, (2) banja likukhala m’dziko limene boma linaletsa nchito yathu yolalikila, (3) munthu akukhala ku malo akutali kwambili komanso ovuta kufikako.